Zefaniya 1:10 BL92

10 Ndipo tsiku ilo, ati Yehova, kudzakhala phokoso lakulira locokera ku cipata cansomba, ndi kucema kocokera ku dera laciwiri, ndi kugamuka kwakukuru kocokera kuzitunda.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 1

Onani Zefaniya 1:10 nkhani