Zefaniya 3:14 BL92

14 Yimba, mwana wamkazi wa Ziyoni; pfuula, Israyeli; kondwera nusekerere ndi mtima wonse, mwana wamkazi wa Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 3

Onani Zefaniya 3:14 nkhani