Zefaniya 3:13 BL92

13 Otsala a Israyeli sadzacita cosalungama, kapena kunena mabodza; ndi m'kamwa mwao simudzapezeka lilime lonyenga; pakuti adzadya nadzagona pansi, ndi palibe wakuwaopsa.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 3

Onani Zefaniya 3:13 nkhani