Zefaniya 3:4 BL92

4 Aneneri ace ndiwo anthu a matukutuku ndi onyenga; ansembe ao anaipsa malo opatulika, napotoza cilamulo.

Werengani mutu wathunthu Zefaniya 3

Onani Zefaniya 3:4 nkhani