5 kuti Vthenga Wabwino wathu sunadza kwa inu m'mau mokha, komatunso mumphamvu, ndi mwa Mzimu Woyera, ndi m'kucuruka kwakukuru; monga mudziwa tinakhala onga otani mwa inu cifukwa ca inu.
Werengani mutu wathunthu 1 Atesalonika 1
Onani 1 Atesalonika 1:5 nkhani