8 Pakuti kuturuka kwa inu kudamveka mau a Ambuye, osati m'Makedoniya ndi Akaya mokha, komatu m'malo monse cikhulupiriro canu ca kwa Mulungu cidaturuka; kotero kuti sikufunika kwa ife kulankhula kanthu.
Werengani mutu wathunthu 1 Atesalonika 1
Onani 1 Atesalonika 1:8 nkhani