3 Pamene angonena, Mtendere ndi mosatekeseka, pamenepo cionongeko cobukapo cidzawagwera, monga zowawa mkazi wa pakati; ndipo sadzapulumuka konse.
Werengani mutu wathunthu 1 Atesalonika 5
Onani 1 Atesalonika 5:3 nkhani