11 Kukatero tikupemphereraninso nthawi zonse, kuti Mulungu wathu akakuyeseni inu oyenera kuitanidwa kwanu, nakakwaniritse comkomera conse, ndi nchito ya cikhulupiriro mumphamvu;
Werengani mutu wathunthu 2 Atesalonika 1
Onani 2 Atesalonika 1:11 nkhani