2 Atesalonika 2:2 BL92

2 kuti musamagwedezeka mtima msanga ndi kutaya maganizo anu, kapena kuopsedwa, mwa mzimu kapena mwa mau; kapena mwa kalata, monga wolembedwa ndi ife, monga ngati tsiku la Ambuye lafika;

Werengani mutu wathunthu 2 Atesalonika 2

Onani 2 Atesalonika 2:2 nkhani