9 ndiye amene kudza kwace kuli monga mwa macitidwe a Satana, mu mphamvu yonse, ndi zizindikilo ndi zozizwa zonama;
Werengani mutu wathunthu 2 Atesalonika 2
Onani 2 Atesalonika 2:9 nkhani