2 Petro 1:12 BL92

12 Mwa ici sindidzaleka kukukumbutsani inu nthawi zonse za izi, mungakhale muzidziwa nimukhazikika m'coonadi ciri ndi inu.

Werengani mutu wathunthu 2 Petro 1

Onani 2 Petro 1:12 nkhani