17 Pakuti analandira kwa Mulungu Atate ulemu ndi ulemerero, pakumdzera iye mao otere ocokera ku ulemerero waukuru, Uyu ndi Mwana wanga wokondedwa, amene Ine ndikondwera naye;
Werengani mutu wathunthu 2 Petro 1
Onani 2 Petro 1:17 nkhani