19 Ndipo tiri nao mau a cinenero okhazikika koposa; amene mucita bwino powasamalira, monga nyali younikira m'malo a mdima, kufikira kukaca, nikauka nthanda pa mtima yanu;
Werengani mutu wathunthu 2 Petro 1
Onani 2 Petro 1:19 nkhani