5 Ndipo mwa ici comwe, pakutengeraponso cangu conse, muonjezerapo ukoma pa cikhulupiriro canu, ndi paukoma cizindikiritso; ndi pacizindikiritso codziletsa;
Werengani mutu wathunthu 2 Petro 1
Onani 2 Petro 1:5 nkhani