2 Petro 2:10 BL92

10 kama makamaka iwo akutsata zathupi, m'cilakolako ca zodetsa, napeputsa cilamuliro; osaopa kanthu, otsata cifuniro ca iwo eni, santhunthumira kucitira mwano akulu;

Werengani mutu wathunthu 2 Petro 2

Onani 2 Petro 2:10 nkhani