14 okhala nao maso odzala ndi cigololo, osakhoza kuleka ucimo, kunyengerera iwo a moyo wosakhazikika; okhala nao mtima wozolowera kusirira; ana a temberero;
Werengani mutu wathunthu 2 Petro 2
Onani 2 Petro 2:14 nkhani