2 Petro 2:19 BL92

19 ndi kuwalonjezera iwo ufulu, pokhala iwo okha ali aka polo a cibvundi; pakuti iye amene munthu agonjedwa naye, ameneyonso adzakhala kapolo wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Petro 2

Onani 2 Petro 2:19 nkhani