9 Ambuye sazengereza nalo lonjezano, monga ena aciyesa cizengerezo; komatu aleza mtima kwa inu, wosafuna kuti ena aonongeke, koma kuti onse afike kukulapa.
Werengani mutu wathunthu 2 Petro 3
Onani 2 Petro 3:9 nkhani