2 Timoteo 2:22 BL92

22 Koma thawa zilakolako za unyamata, nutsate cilungamo, cikhulupiriro, cikondi, mtendere, pamodzi ndi iwo akuitana pa Ambuye ndi mitima yoyera.

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 2

Onani 2 Timoteo 2:22 nkhani