2 Timoteo 3:8 BL92

8 Ndipo monga momwe Yane ndi Yambre anatsutsana naye Mose, kotero iwonso atsutsana naco coonadi; ndiwo anthu obvunditsitsa mtima, osatsimikizidwa pacikhulupiriro.

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 3

Onani 2 Timoteo 3:8 nkhani