2 Timoteo 4:1 BL92

1 Ndikucitira umboni pamaso pa Mulungu ndi Kristu Yesu, amene adzaweruza amoyo ndi akufa, ndi pa maonekedwe ace ndi ufumu wace;

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 4

Onani 2 Timoteo 4:1 nkhani