2 Timoteo 4:17 BL92

17 Koma Ambuye anaima nane nandipatsa mphamvu; kuti mwa ine cilalikiro cimveke konse konse, ndi amitundu onse amve; ndipo ndinalanditsidwa m'kamwa mwa mkango.

Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 4

Onani 2 Timoteo 4:17 nkhani