3 Pakuti idzafika nthawi imene sadzalola ciphunzitso colamitsa; komatu poyabwa m'khutu adzadziuniikitsa aphunzitsi monga mwa zilakolako za iwo okha:
Werengani mutu wathunthu 2 Timoteo 4
Onani 2 Timoteo 4:3 nkhani