27 Pakutinso anadwaladi pafupi imfa; komatu Mulungu anamcitira cifundo; koma si iye yekha, komatu inenso, kuti ndisakhale naco cisoni cionjezere-onjezere.
Werengani mutu wathunthu Afilipi 2
Onani Afilipi 2:27 nkhani