9 Zimenenso mudaziphunzira, ndi kuzilandira, ndi kuzimva, ndi kuziona mwa ine, zomwezo citani; ndipo Mulungu wa mtendere adzakhala pamodzi ndi inu.
Werengani mutu wathunthu Afilipi 4
Onani Afilipi 4:9 nkhani