Akolose 1:18 BL92

18 Ndipo iye ali mutu wa thupi, Eklesiayo; ndiye ciyambi, wobadwa woyamba woturuka mwa akufa; kuti akakhale iye mwa zonse woyambayamba.

Werengani mutu wathunthu Akolose 1

Onani Akolose 1:18 nkhani