16 Abvomereza kuti adziwa Mulungu, koma ndi Debito zao amkana iye, popeza ali onyansitsa, ndi osamvera, ndi pa nchito zonse zabwino osatsimikizidwa.
Werengani mutu wathunthu Tito 1
Onani Tito 1:16 nkhani