2 asacitire mwano munthu ali yense, asakhale andeu, akhale aulere, naonetsere cifatso conse pa anthu onse.
Werengani mutu wathunthu Tito 3
Onani Tito 3:2 nkhani