Malaki 1:7 BL92

7 Mupereka mkate wodetsedwa pa guwa langa la nsembe; ndipo mukuti, Takudetsani motani? M'menemo, mwakuti munena, Gome la Yehova nlonyozeka.

Werengani mutu wathunthu Malaki 1

Onani Malaki 1:7 nkhani