3 Ndipo mudzapondereza oipa; pakuti adzakhala ngati mapulusa ku mapazi anu, tsiku ndidzaikalo, ati Yehova wamakamu.
Werengani mutu wathunthu Malaki 4
Onani Malaki 4:3 nkhani