Malaki 4:6 BL92

6 Ndipo adzabwezera mitima ya atate kwa ana, ndi mitima ya ana kwa atate ao; kuti ndisafike ndi kukantha dziko lionongeke konse.

Werengani mutu wathunthu Malaki 4

Onani Malaki 4:6 nkhani