11 Anthu ace onse ausa moyo nafunafuna mkate;Ndi zokondweretsa zao agula zakudya kuti atsitsimutse moyo wao;Taonani, Yehova, nimupenye; pakuti ndasanduka wonyansa.
Werengani mutu wathunthu Maliro 1
Onani Maliro 1:11 nkhani