Maliro 1:9 BL92

9 Udio wace unali m'nsaru zace; sunakumbukira citsiriziro cace;Cifukwa cace watsika mozizwitsa; ulibe wakuutonthoza;Taonani Yehova, msauko wanga, pakuti mdaniyo wadzikuzayekha.

Werengani mutu wathunthu Maliro 1

Onani Maliro 1:9 nkhani