Maliro 2:14 BL92

14 Aneneri ako anakuonera masomphenya acabe ndi opusa;Osaulula mphulupulu yako kuti abweze undende wako,Koma anakuonera manenero acabe ndi opambutsa.

Werengani mutu wathunthu Maliro 2

Onani Maliro 2:14 nkhani