22 Cifukwa cakusathedwa ife ndico cifundo ca Yehova, pakuti cisoni cace sicileka;
Werengani mutu wathunthu Maliro 3
Onani Maliro 3:22 nkhani