Maliro 4:22 BL92

22 Mphulupulu yako yatha, mwana wamkazi wa Ziyoni, Yehova sadzakutenganso ndende;Koma adzazonda mphulupulu yako, mwana wa mkazi wa Edomu, nadzabvumbulutsa zocimwa zako.

Werengani mutu wathunthu Maliro 4

Onani Maliro 4:22 nkhani