Maliro 4:6 BL92

6 Pakuti mphulupulu ya mwana wamkazi wa anthu amtundu wanga, ikula koposa cimo la Sodomu,Umene unapasuka m'kamphindi, anthu osaucitira kanthu.

Werengani mutu wathunthu Maliro 4

Onani Maliro 4:6 nkhani