19 Inu, Yehova, mukhala cikhalire,Ndi mpando wanu wacifumu ku mibadwo mibadwo.
20 Bwanji mutiiwala ciiwalire,Ndi kutisiya masiku ambirimbiri;
21 Mutitembenuzire kwa Inu, Yehova, ndipo tidzatembenuzidwadi,Mukonzenso masiku athu ngati kale lija.
22 Koma mwatikaniza konse,Mwatikwiyira kopambana.