Mika 2:1 BL92

1 Tsoka iwo akulingirira cinyengo, ndi kukonza coipa pakama pao! kutaca m'mawa acicita, popeza cikhozeka m'manja mwao.

Werengani mutu wathunthu Mika 2

Onani Mika 2:1 nkhani