16 Udziyeseze wadazi, udzimete wekha cifukwa ca ana ako okondwera nao; kuza dazi lako ngati la muimba; pakuti anakucokera, nalowa ndende.
Werengani mutu wathunthu Mika 1
Onani Mika 1:16 nkhani