Mika 3:4 BL92

4 Pamenepo adzapfuulira kwa Yehova, koma sadzawayankha; inde, adzawabisira nkhope yace nthawi yomweyo, monga momwe anaipsa macitidwe ao.

Werengani mutu wathunthu Mika 3

Onani Mika 3:4 nkhani