5 Atero Yehova za aneneriakulakwitsa anthu anga; akuluma ndi mano ao, ndi kupfuula, Mtendere; ndipo, ali yense wosapereka m'kamwa mwao, amkonzera nkhondo;
Werengani mutu wathunthu Mika 3
Onani Mika 3:5 nkhani