Mika 7:17 BL92

17 Adzanyambita pfumbi ngati njoka; ngati zokwawa za padziko, adzanjenjemera poturuka m'ngaka mwao; adzafika kwa Yehova Mulungu wao ndi mantha, nadzaopa cifukwa ca iwe.

Werengani mutu wathunthu Mika 7

Onani Mika 7:17 nkhani