Mika 7:18 BL92

18 Ndani Mulungu wofanana ndi Inu, wakukhululukira mphulupulu, wakupitirira zolakwa za otsala a colowa cace? sasunga mkwiyo wace ku nthawi yonse popeza akondwera naco cifundo.

Werengani mutu wathunthu Mika 7

Onani Mika 7:18 nkhani