Mika 7:2 BL92

2 Watha wacifundo m'dziko, palibe woongoka mwa anthu; onsewo alalira mwazi; yense asaka mbale wace ndi ukonde.

Werengani mutu wathunthu Mika 7

Onani Mika 7:2 nkhani