1 Ndipo Naomi anali nave mbale wa mwamuna wace, ndiye munthu mwini cuma cambiri wa banja la Elimeleki; dzina lace ndiye Boazi.
Werengani mutu wathunthu Rute 2
Onani Rute 2:1 nkhani