Rute 3:1 BL92

1 Pamenepo Naomi mpongozi wace ananena naye, Mwana wanga, kodi ndisakufunire popumulako, kuti ukhale bwino?

Werengani mutu wathunthu Rute 3

Onani Rute 3:1 nkhani