Yoweli 3:8 BL92

8 ndipo ndidzagulitsa ana ako amuna ndi akazi m'dzanja la ana a Yuda; ndipo iwo adzawagulitsa kwa anthu a Seba, kwa anthu okhala kutari; pakuti Yehova wanena.

Werengani mutu wathunthu Yoweli 3

Onani Yoweli 3:8 nkhani