1 Atesalonika 2:9 BL92

9 Pakuti mukumbukila, abale, cigwiritso cathu ndi cibvuto cathu; pocita usiku ndi usana, kuti tingalemetse wina wa inu, tinalalikira kwa inu Uthenga Wabwino wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu 1 Atesalonika 2

Onani 1 Atesalonika 2:9 nkhani