1 Petro 5:1 BL92

1 Akulu tsono mwa inu ndiwadandaulira, ine mkulu mnzanu ndi mboni ya zowawa za Kristu, ndinenso wolawana nao ulemerero udzabvumbulutsikawo:

Werengani mutu wathunthu 1 Petro 5

Onani 1 Petro 5:1 nkhani